Ezara 10:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuti ali yense wosafikako atapita masiku atatu, monga mwa uphungu wa akalonga ndi akuru, cuma cace conse cidzaonongeka konse, ndipo iye adzacotsedwa ku msonkhano wa iwo otengedwa ndende.

Ezara 10

Ezara 10:4-13