Ezara 10:42-44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

42. Salumu, Amariya, Yosefe.

43. A ana a Nebo: Yeieli, Matitiya, Zabadi, Zebina, Ido, ndi Yoeli, Banaya,

44. Awa onse adatenga akazi acilendo, ndi ena a iwowa anali ndi akazi amene adawabalira ana.

Ezara 10