Estere 9:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace anacha masikuwa Purimu, ndilo dzina la ulawo. Momwemo, cifukwa ca mau onse a kalatayo, ndi izi adaziona za mlanduwo, ndi ici cidawadzera,

Estere 9

Estere 9:18-32