Estere 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanenanso Estere pamaso pa mfumu, nagwa ku mapazi ace, nalira misozi, nampembedza kuti acotse coipaco ca Hamani wa ku Agagi, ndi ciwembu adacipangira Ayuda,

Estere 8

Estere 8:1-6