Estere 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ngati mfumu indikomera mtima, ngatinso cakomera mfumu kupereka pempho langa ndi kucita cofuna ine, adze mfumu ndi Hamani ku madyerero ndidzawakonzera; ndipo mawa ndidzacita monga yanena mfumu.

Estere 5

Estere 5:1-13