Estere 5:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ninena naye mfumu, Mufunanji, Estere mkazi wamkuru? pempho lanu nciani? lidzaperekedwa kwa inu, kufikira limodzi la magawo awiri a ufumuwo.

Estere 5

Estere 5:1-11