Estere 3:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anyamata onse a mfumu okhala m'cipata ca mfumu anamweramira, namgwadira Hamani; pakuti mfumu idalamulira cotero za iye. Koma Moredekai sanamweramira kapena kumgwadira.

Estere 3

Estere 3:1-9