Eksodo 8:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku ilo ndidzalemba malire dziko la Goseni, m'mene mukhala anthu anga, kuti pamenepo pasakhale mizaza; kotero kuti udziwe kuti Ine ndine Yehova pakati pa dzikoli.

Eksodo 8

Eksodo 8:19-24