Eksodo 7:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Koma Aaigupto onse anakumba m'mphepete mwa nyanja kufuna madzi akumwa; pakuti sanakhoza kumwa madzi a m'nyanjamo.

25. Ndipo anafikiramasiku asanu ndi awiri atapanda nyanja Yehova.

Eksodo 7