Eksodo 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndamvanso kubuula kwa ana a Israyeli, amene Aaigupto awayesa akapolo; ndipo ndakumbukila cipangano canga.

Eksodo 6

Eksodo 6:1-7