Eksodo 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananena kwa Mose, Tsopano udzaona comwe ndidzacitira Farao; pakuti ndi dzanja lamphamvu adzawalola apite, inde ndi dzanja lamphamvu adzawaingitsa m'dziko lace.

Eksodo 6

Eksodo 6:1-11