Eksodo 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Farao anati, Yehova ndani, kuti ndimvere mau ace ndi kulola Israyeli apite? Sindimdziwa Yehova, ndiponso sindidzalola Israyeli apite.

Eksodo 5

Eksodo 5:1-7