Eksodo 5:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akapitao a ana a Israyeli anaona kuti kudawaipira, pamene ananena, Musamacepetsa njerwa zanu, nchito ya tsiku pa tsiku lace.

Eksodo 5

Eksodo 5:11-23