Eksodo 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Zipora anatenga mpeni wamwala, nadula khungu la mwana wace, naliponya pa mapazi ace; nati, Pakuti iwe ndiwe mkwati wanga wamwazi. Ndipo iye anamleka.

Eksodo 4

Eksodo 4:20-31