Eksodo 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova ananena naye, Anampangira munthu m'kamwa ndani? Kapena analenga munthu wosalankhula ndani, kapena wogontha, kapena wamaso, kapena wakhungu? Si ndine Yehova kodi?

Eksodo 4

Eksodo 4:9-19