Eksodo 39:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaomba capacifuwa, nchito ya mmisiri, monga maombedwe ace a efodi; ca golidi, lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.

Eksodo 39

Eksodo 39:1-12