Eksodo 39:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga miriu ya golidi woona, napakiza miriu ndi makangaza, pa mkawo wa mwinjiro pozungulira, popakiza ndi makangaza.

Eksodo 39

Eksodo 39:15-32