Eksodo 38:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo matalente zana limodzi a siliva ndiwo a kuyengera makamwa a malo opatulika, ndi makamwa a nsaru yocinga; makamwa zana limodzi matalente zana limodzi, talente limodzi kamwa limodzi.

Eksodo 38

Eksodo 38:20-31