Eksodo 36:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose analamulira, ndipo anamveketsa mau mwa cigono conse, ndi kuti, Asaonjezere nchito ya ku copereka ca malo opatulika, ngakhale mwamuna ngakhale mkazi. Tero anawaletsa anthu asabwere nazo zina.

Eksodo 36

Eksodo 36:3-13