Eksodo 36:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Utali wace wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwace kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu.

Eksodo 36

Eksodo 36:20-31