Eksodo 33:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose akatenga cihemaco nacimanga kunja kwa cigono, kutari kwa cigono; nacicha, Cihema cokomanako. Ndipo kunakhala kuti yense wakufuna Yehova anaturuka kumka ku cihema cokomanako kunja kwa cigono.

Eksodo 33

Eksodo 33:1-17