Eksodo 32:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

wapatuka msanga njira imene ndinawauza; wadzinyengera mwana wa ng'ombe, namgwadira, namphera nsembe, nati, Siyi milungu yako, Israyeli, imene inakukweza kucokera m'dziko la Aigupto,

Eksodo 32

Eksodo 32:1-17