Eksodo 32:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza Mose adati, Mdzazireni Yehova manja anu lero, pakuti yense akhale mdani wa mwana wace wamwamuna, ndi mdani wa mbale wace; kuti akudalitseni lero lino.

Eksodo 32

Eksodo 32:21-35