Eksodo 32:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Ndipo Yehova analeka coipa adanenaci, kuwacitira anthu ace.

15. Ndipo Mose anatembenuka, natsika m'phirimo, magome awiri a mboni ali m'dzanja lace; magome olembedwa kwina ndi kwina; analembedwa mbali yina ndi inzace yomwe.

16. Ndipo magomewo ndiwo nchito ya Mulungu, kulembaku ndiko kulemba kwa Mulungu, kozokoteka pa magomewo.

Eksodo 32