Eksodo 32:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anapemba kwa Yehova Mulungu wace, nati, Yehova, mtima wanu upserenji pa anthu anu, amene munawaturutsa m'dziko la Aigupto ndi mphamvu yaikuru, ndi dzanja lolimba?

Eksodo 32

Eksodo 32:10-20