Eksodo 31:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndico cizindikilo cosatha pakati pa Ine ndi ana a Israyeli; pakuti Yehova analenga zam'mwamba ndi dziko lapansi masiku asanu ndi limodzi, napumula tsiku lacisanu ndi ciwiri, naonanso mphamvu.

Eksodo 31

Eksodo 31:9-18