Eksodo 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ananenanso Ine ndine Mulungu wa atate wako, Molungu wa Abrahamu, Molungu wa Isake, ndi Mulungu wa Yakobo. Ndipo Mose anabisa nkhope yace; popeza anaopa kuyang'ana Mulungu,

Eksodo 3

Eksodo 3:1-10