Eksodo 29:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo utenge zobvalazo ndi kubveka Aroni maraya am'kati, ndi mwinjiro wa efodi, ndi efodi, ndi capacifuwa, ndi kummangira m'cuuno ndi mpango wa efodi woluka mwanzeru;

Eksodo 29

Eksodo 29:1-10