Eksodo 29:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mwana wace wamwamuna amene adzakhala wansembe m'malo mwace azibvala masiku asanu ndi awiri, pakulowa iye m'cihema cokomanako kutumikira m'malo opatulika.

Eksodo 29

Eksodo 29:20-37