Eksodo 29:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo upatule nganga va nsembe yoweyula, ndi mwendo wam'mwamba wa nsembe yokweza, imene anaiweyula, ndi imene anaikweza, za nkhosa yamphongo yakudzaza manja; ziri za Aroni, ndi za ana ace amuna;

Eksodo 29

Eksodo 29:19-37