Eksodo 29:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nuiphe nkhosa yamphongoyo, ndi kutenga mwazi wace, ndi kuuwaza pa guwa la nsembe pozungulira.

Eksodo 29

Eksodo 29:6-17