Eksodo 29:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo utapeko pa mwazi wa ng'ombe yamphongo, ndi kuupaka pa nyanga za guwa la nsembe ndi cala cako, nutsanulire mwazi wonse pa tsinde la guwa la nsembe.

Eksodo 29

Eksodo 29:3-16