Eksodo 28:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo polowa mutu pakhale pakati pace; pakhale mkawo pozungulira polowa pace, wa nchito yoomba, ngati polowa pa malaya ociniiriza, pangang'ambike.

Eksodo 28

Eksodo 28:22-35