Eksodo 28:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ulike miyala iwiriyo pa zapamapewa za efodi, ikhale miyala ya cikumbutso ca ana a Israyeli; ndipo Aroni azinyamula maina ao pa mapewa ace awiri, akhale cikumbutso pamaso pa Yehova.

Eksodo 28

Eksodo 28:5-14