Eksodo 26:26-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Ndipo uzipanga mitanda ya mtengo wasitimu; isanu ya matabwa a pa mbali yina ya kacisi,

27. ndi mitanda isanu ya matabwa a Pel mbali yina ya kacisi, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya kacisi ya kumbuyo kumadzulo.

28. Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo.

Eksodo 26