Eksodo 26:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nuzipanga makamwa makumi anai asiliva pansi pa matabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yace iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yace iwiri;

Eksodo 26

Eksodo 26:13-21