Eksodo 26:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mkono wa pa mbali yino, ndi mkono wa pa mbali inzace, wakutsalira m'utali wace wa nsaru za hemalo, icinge pambali zace za kacisi, mbali yino ndi mbali yina, kumphimba.

Eksodo 26

Eksodo 26:12-16