Eksodo 26:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uziika magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru imodzi, ya kuthungo ya cilumikizano, ndi magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru ya kuthungo ya cilumikizano cina.

Eksodo 26

Eksodo 26:2-20