Eksodo 24:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa akuru, Tilindeni kuno kufikira tidzabwera kwa inu; ndipo taonani, Aroni ndi Huri ali nanu; munthu akakhala ndi mlandu abwere kwa iwowa.

Eksodo 24

Eksodo 24:9-18