Eksodo 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akadyetsa coweta pabusa kapena pa munda wamphesa, atamasula coweta cace, ndipo citadya podyetsa pa mwini wace; alipe podyetsa pace poposa, ndi munda wa mphesa wace woposa.

Eksodo 22

Eksodo 22:1-6