Eksodo 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akaikiza buru, kapena ng'ombe, kapena nkhosa, kapena coweta cina kwa mnansi wace, ndipo cikafa, kapena ciphwetekwa, kapena wina acipitikitsa osaciona munthu;

Eksodo 22

Eksodo 22:1-18