Eksodo 22:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akaba ng'ombe, kapena nkhosa, nakaipha, kapena kuigulitsa, azilipa ng'ombe zisanu pa ng'ombeyo; ndi nkhosa zinai pa nkhosayo,

Eksodo 22

Eksodo 22:1-3