Eksodo 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

usazipembedzere izo, usazitumikire izo; cifukwa Ine Yehova Mulungu wako ndiri Mulungu wansanje, wakulanga ana cifukwa ca atate ao, kufikira mbadwo wacitatu ndi wacinai wa iwo amene akudana ndi Ine;

Eksodo 20

Eksodo 20:2-11