Eksodo 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene sanathe kumbisanso, anamtengera kabokosi kagumbwa, napakapo nkhunga ndi phula; naikamo mwanayo, nakaika pakati pa mabango m'mbali mwa nyanja.

Eksodo 2

Eksodo 2:1-9