Eksodo 18:26-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Ndipo anaweruza anthu nthawi zonse; mlandu wakuwalaka amabwera nao kwa Mose, ndi milandu yaing'ono yonse amaweruza okha.

27. Ndipo Mose analola mpongozi wace amuke; ndipo anacoka kumka ku dziko lace.

Eksodo 18