Eksodo 18:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yetero, wansembe wa Midyani, mpongozi wa Mose, anamva zonse zimene Mulungu adacitira Mose ndi Israyeli anthu ace, kuti Yehova adaturutsa Israyeli m'Aigupto.

Eksodo 18

Eksodo 18:1-11