Eksodo 17:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anthu anatsutsana ndi Mose, nati, Tipatseni madzi timwe, Koma Mose ananena nao, Mutsutsana nane bwanji? Muyeseranji Yehova?

Eksodo 17

Eksodo 17:1-10