Eksodo 16:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anadya mana zaka makumi anai, kufikira atalowa dziko la midzi; anadya mana kufikira analowa malire a dziko la Kanani.

Eksodo 16

Eksodo 16:29-36