Eksodo 16:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sanammvera Mose; ndipo ena anasiyako kufikira m'mawa; koma unagwa mphutsi, nununkha. Ndipo Mose anakwiya nao.

Eksodo 16

Eksodo 16:19-28