Eksodo 16:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anayesa ndi omeri, iye amene adaola wambiri sunamtsalira, ndi iye amene adaola pang'ono sunamsowa; yense anaola monga mwa njala yace.

Eksodo 16

Eksodo 16:17-26